Genesis 43:22 - Buku Lopatulika22 Ndalama zina tatenga m'manja mwathu kuti tigule chakudya: sitimdziwa amene anaika ndalama zathu m'matumba athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndalama zina tatenga m'manja mwathu kuti tigule chakudya: sitimdziwa amene anaika ndalama zathu m'matumba athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ndipo tabwera nazonso ndalama zina zodzagulira chakudya china. Amene adaika ndalama m'matumba mwathu, sitikumudziŵa ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Tabweretsanso ndalama zina kuti tigule chakudya. Sitikudziwa kuti kaya ndani anayika ndalamazo mʼmatumba athu.” Onani mutuwo |