Genesis 43:17 - Buku Lopatulika17 Munthuyo anachita monga anamuuza Yosefe, ndipo munthuyo analowa nao anthuwo m'nyumba ya Yosefe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Munthuyo anachita monga anamuuza Yosefe, ndipo munthuyo analowa nao anthuwo m'nyumba ya Yosefe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Wantchitoyo adachita monga momwe Yosefe adamuuzira, napita nawo abale aja kunyumba kwa Yosefe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Wantchitoyo anachita monga momwe Yosefe ananenera, ndipo anawatengera abale aja ku nyumba kwa Yosefe. Onani mutuwo |