Genesis 42:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo ana aamuna a Israele anadza kudzagula mwa iwo amene anadzako, pakuti m'dziko la Kanani munali njala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo ana amuna a Israele anadza kudzagula mwa iwo amene anadzako, pakuti m'dziko la Kanani munali njala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ana a Israelewo adapita ku Ejipito kukagula chakudya pamodzi ndi anthu ena onse, chifukwa chakuti ku dziko la Kanani kunali njala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Choncho ana a Israeli aja anapita pamodzi ndi gulu la anzawo kukagula tirigu pakuti ku Kanaani kunalinso njala. Onani mutuwo |