Genesis 42:4 - Buku Lopatulika4 Koma Yakobo sanamtume Benjamini mphwake wa Yosefe, pamodzi ndi abale ake, chifukwa anati, Choipa chingam'gwere iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma Yakobo sanamtume Benjamini mphwake wa Yosefe, pamodzi ndi abale ake, chifukwa anati, Choipa chingam'gwere iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Yakobe sadamtume nawo Benjamini, mng'ono wake weniweni wa Yosefe uja, chifukwa ankaopa kuti angapeze tsoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma Yakobo sanamulole Benjamini mngʼono wake wa Yosefe kuti apite nawo chifukwa anaopa kuti choyipa chingamuchitikire. Onani mutuwo |