Genesis 42:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo abale ake a Yosefe khumi anatsikira kukagula tirigu mu Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo abale ake a Yosefe khumi anatsikira kukagula tirigu m'Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Motero abale ake a Yosefe khumi adanyamuka kupita ku Ejipito kukagula tirigu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho abale ake khumi a Yosefe anapita kukagula tirigu ku Igupto. Onani mutuwo |