Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 42:32 - Buku Lopatulika

32 tili abale khumi ndi awiri, ana a atate wathu; wina palibe, ndipo lero wamng'ono ali ndi atate wathu m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 tili abale khumi ndi awiri, ana a atate wathu; wina palibe, ndipo lero wamng'ono ali ndi atate wathu m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Ife tonse tinalipo ana aamuna khumi ndi aŵiri, koma mmodzi adamwalira, ndipo wamng'ono ali ndi bambo wathu ku Kanani.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ife tonse tinalipo ana aamuna khumi ndi awiri, abambo mmodzi. Mmodzi anamwalira, ndipo wamngʼono ali ndi abambo athu ku Kanaani.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 42:32
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anabwera kwa abale ake, nati, Mwana palibe; ndipo ine ndipita kuti?


Nati iwo, Akapolo anu ndife abale khumi, ana aamuna a munthu mmodzi m'dziko la Kanani; ndipo, taonani, wamng'ono ali ndi atate wathu lero; ndipo palibe mmodzi.


Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda;


Ndipo munthuyo mwini dziko anati kwa ife, Momwemu ndidzadziwa kuti muli anthu oona; siyani mmodzi wa abale anu pamodzi ndi ine, tengani tirigu wa njala ya kwanu, mukani;


Apo pali Benjamini wamng'ono, wakuwachita ufumu, akulu a Yuda, ndi a upo wao, akulu a Zebuloni, akulu a Nafutali.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa