Genesis 42:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo munthuyo mwini dziko anati kwa ife, Momwemu ndidzadziwa kuti muli anthu oona; siyani mmodzi wa abale anu pamodzi ndi ine, tengani tirigu wa njala ya kwanu, mukani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo munthuyo mwini dziko anati kwa ife, Momwemu ndidzadziwa kuti muli anthu oona; siyani mmodzi wa abale anu pamodzi ndi ine, tengani tirigu wa njala ya kwanu, mukani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Pamenepo iyeyo adati, ‘Kuti ndidziŵe kuti ndinu anthu okhulupirika, mmodzi mwa inu atsale ndi ine kuno, koma ena nonsenu mutenge tirigu, mupite naye ku banja la kwanu kuli njalako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ndipo nduna ija inati kwa ife, “Kuti ndidziwedi kuti ndinu anthu owona mtima muchite izi: Mmodzi mwa inu atsale ndi ine kuno, ndipo enanu mutenge chakudya ndi kubwerera kwanu kumene kuli njalako. Onani mutuwo |