Genesis 42:31 - Buku Lopatulika31 Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ife tidamuuza munthuyo kuti, ‘Ndife anthu okhulupirika, osati azondi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Koma tinamuwuza kuti, ‘Ndife anthu woona mtima osati akazitape. Onani mutuwo |