Genesis 42:30 - Buku Lopatulika30 kuti, Munthu mwini dziko, ananena ndi ife mwankhalwe, natiyesa ife ozonda dziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 kuti, Munthu mwini dziko, ananena ndi ife mwankhalwe, natiyesa ife ozonda dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 “Nduna yaikulu ya dzikolo idatilankhula mozaza, kuti ati ndife ozonda dziko laolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 “Nduna yayikulu ya mʼdzikomo inatiyankhula mwa ukali kwambiri ndipo inkatiyesa kuti ndife akazitape. Onani mutuwo |