Genesis 42:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo sanadziwe kuti Yosefe anamva; chifukwa anali ndi womasulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo sanadziwe kuti Yosefe anamva; chifukwa anali ndi womasulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yosefe anali kumva zonse zimene ankakambiranazo, koma iwowo sadadziŵe, chifukwa choti ankalankhula naye kudzera mwa womasulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Koma sanadziwe kuti Yosefe ankawamva popeza kuti ankagwiritsa ntchito wotanthauzira poyankhula naye. Onani mutuwo |