Genesis 42:19 - Buku Lopatulika19 ngati muli oona, mmodzi wa abale anu amangidwe m'kaidi momwemo; mukani inu, mupite naye tirigu wa njala ya mabanja anu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ngati muli oona, mmodzi wa abale anu amangidwe m'kaidi momwemo; mukani inu, mupite naye tirigu wa njala ya mabanja anu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ngati ndinu okhulupirika, mmodzi yekha atsalire m'ndendemu, ena nonsenu mungathe kupita, kuti mukapereke tirigu mwagulayu ku banja la kwanu kuli njalako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ngati muli anthu achilungamo, mmodzi wa inu atsale mʼndende, pamene ena nonse mupite kwanu kuti muwatengere chakudya anthu akwanu kuli njalako. Onani mutuwo |