Genesis 42:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yosefe anati kwa iwo tsiku lachitatu, Chitani ichi, kuti mukhale ndi moyo; ine ndiopa Mulungu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yosefe anati kwa iwo tsiku lachitatu, Chitani ichi, kuti mukhale ndi moyo; ine ndiopa Mulungu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Patapita masiku atatu, adaŵauza kuti, “Ine ndimaopa Mulungu. Choncho ndikupatsani mwai woupulumutsa moyo wanu mukachita izi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pa tsiku lachitatu Yosefe anawawuza kuti, “Popeza ine ndimaopa Mulungu, ndipo inuyo ngati mukufuna kukhala ndi moyo muchite izi: Onani mutuwo |