Genesis 42:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Yosefe anati kwa iwo, Ndicho chimene ndinakunenani inu, kuti, Ndinu ozonda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Yosefe anati kwa iwo, Ndicho chimene ndinakunenani inu, kuti, Ndinu ozonda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Koma Yosefe adaŵayankha kuti, “Paja ndanena kale kuti ndinu azondi basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Yosefe anawawuza kuti, “Ndi momwe ndaneneramo: Inu ndinu akazitape. Onani mutuwo |