Genesis 42:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo anaona Yakobo kuti mu Ejipito munali tirigu, nati Yakobo kwa ana ake aamuna, Chifukwa chanji mulinkuyang'anana? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo anaona Yakobo kuti m'Ejipito munali tirigu, nati Yakobo kwa ana ake amuna, Chifukwa chanji mulinkuyang'anana? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yakobe atamva kuti ku Ejipito ndiko kuli tirigu, adafunsa ana ake kuti, “Chifukwa chiyani mukungokhala osachitapo kanthu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yakobo atamva kuti ku Igupto kuli tirigu, anati kwa ana ake, “Nʼchifukwa chiyani mukungoyangʼanana wina ndi mnzake? Onani mutuwo |