Genesis 41:50 - Buku Lopatulika50 Ndipo kwa Yosefe anabadwa ana aamuna awiri, chisanafike chaka cha njala, amene Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni anambalira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Ndipo kwa Yosefe anabadwa ana amuna awiri, chisanafike chaka cha njala, amene Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni anambalira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Zaka zanjala zisanafike, Yosefe adabereka ana aamuna aŵiri mwa Asenati uja, mwana wa Potifera, wansembe wa ku Oni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Zisanafike zaka zanjala, Yosefe anabereka ana aamuna awiri mwa Asenati mwana wa mkazi wa Potifara, wansembe wa Oni. Onani mutuwo |