Genesis 41:44 - Buku Lopatulika44 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Ine ndine Farao, ndipo popanda iwe palibe munthu aliyense adzatukula dzanja lake kapena mwendo wake m'dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Ine ndine Farao, ndipo popanda iwe palibe munthu aliyense adzatukula dzanja lake kapena mwendo wake m'dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Farao adauza Yosefe kuti, “Pali ine ndemwe Farao, iwe ukapanda kulola, palibe ndi mmodzi yemwe amene adzathe kuchita kanthu kalikonse ngakhale kuyenda kumene m'dziko la Ejipito lonseli.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Kenaka Farao anati kwa Yosefe, “Ine ndine Farao; tsono iwe ukapanda kulamula, palibe amene akhoza kuchita chilichonse ngakhale kuyenda kumene mʼdziko lonse la Igupto.” Onani mutuwo |