Genesis 41:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo Farao anamutcha dzina la Yosefe Zafenati-Panea; ndipo anampatsa akwatire Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni. Ndipo Yosefe anatuluka wolamulira, nayendayenda m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo Farao anamutcha dzina la Yosefe Zafenati-Panea; ndipo anampatsa akwatire Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni. Ndipo Yosefe anatuluka wolamulira, nayendayenda m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Pamenepo Yosefe uja adamutcha Zafenati-Panea. Ndipo adampatsa mkazi dzina lake Asenati, mwana wa Potifera amene anali wansembe wa mzinda wa Oni. Choncho Yosefeyo adayendera dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Farao anamupatsa Yosefe dzina lakuti Zafenati-Panea ndipo anamupatsanso Asenati mwana wa mkazi wa Potifara, wansembe wa Oni, kuti akhale mkazi wake. Choncho Yosefe anayendera dziko lonse la Igupto. Onani mutuwo |