Genesis 41:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Taona, ndakhazika iwe wolamulira dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Taona, ndakhazika iwe wolamulira dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Tsono Farao adauzanso Yosefe kuti, “Tsopano ine ndakusankhula iweyo kuti ukhale nduna yaikulu ya dziko lonse la Ejipito.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Choncho Farao anati kwa Yosefe, “Ine ndikukuyika iwe kukhala nduna yoyangʼanira dziko lonse la Igupto.” Onani mutuwo |