Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 41:31 - Buku Lopatulika

31 ndipo zochuluka sizidzazindikirika chifukwa cha njala ikudza m'mbuyoyo, pakuti idzavuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 ndipo zochuluka sizidzazindikirika chifukwa cha njala ikudza m'mbuyoyo, pakuti idzavuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Zaka zonse zija za dzinthu dzambiri sizidzakumbukikanso, chifukwa njala imene idzabwereyo idzakhala yoopsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Zakudya zochuluka za mʼdzikomo zija sizidzakumbukirikanso chifukwa njala imene iti idzabwereyo idzakhala yoopsa.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 41:31
4 Mawu Ofanana  

ndipo pambuyo pao zidzauka zaka zisanu ndi ziwiri za njala; ndipo anthu adzaiwala zochuluka zonsezo m'dziko la Ejipito; ndipo njala idzapululutsa dziko;


Ndipo lotolo linabwerezedwa kawiri kwa Farao, chifukwa chinthu chili chokhazikika ndi Mulungu, ndipo Mulungu afulumira kuchichita.


Dziko lapansi lidzachita dzandidzandi, ngati munthu woledzera, ndi kunjenjemera, ngati chilindo; ndi kulakwa kwake kudzalilemera, ndipo lidzagwa losaukanso.


Koma Yehova anavuta iwo a ku Asidodi ndi dzanja lake, nawaononga, nawazunza ndi mafundo, mu Asidodi ndi m'midzi yake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa