Genesis 41:29 - Buku Lopatulika29 Taonani, zidzafika zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka chakudya m'dziko lonse la Ejipito; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Taonani, zidzafika zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka chakudya m'dziko lonse la Ejipito; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Padzakhala zaka zisanu ndi ziŵiri za dzinthu dzambiri m'dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Zaka zisanu ndi ziwiri za zokolola zochuluka zikubwera mu dziko lonse la Igupto, Onani mutuwo |