Genesis 41:28 - Buku Lopatulika28 Ichi ndi chinthu chimene ndinena kwa Farao: chimene Mulungu ati achite wasonyeza kwa Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ichi ndi chinthu chimene ndinena kwa Farao: chimene Mulungu ati achite wasonyeza kwa Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono monga momwe ndanenera, ndiye kuti Mulungu wakuuziranitu zomwe adzachite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 “Tsono ndi monga ndafotokozeramu kuti Mulungu wakuwuziranitu zimene adzachite. Onani mutuwo |