Genesis 41:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Farao ananena kwa Yosefe, M'loto langa taona, ndinaima m'mphepete mwa mtsinje; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Farao ananena kwa Yosefe, M'loto langa taona, ndinaima m'mphepete mwa nyanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Apo Farao adati, “Ine ndidaalota ntaimirira pamphepete pa mtsinje wa Nailo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, “Ndinalota nditayimirira mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo, Onani mutuwo |