Genesis 41:18 - Buku Lopatulika18 ndipo taona, zinatuluka m'mtsinjemo ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri, zonenepa ndi za maonekedwe abwino; ndipo zinadya m'mabango; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndipo taona, zinatuluka m'nyanjamo ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri, zonenepa ndi za maonekedwe abwino; ndipo zinadya m'mabango; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Nthaŵi yomweyo ndidangoona ng'ombe zisanu ndi ziŵiri zonenepa bwino zitatuluka mumtsinjemo, nkuyamba kudya msipu wam'mabango. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 ndipo ngʼombe zisanu ndi ziwiri zonenepa ndi zooneka bwino zinatuluka mu mtsinje muja ndi kumadya msipu wa mu mawango. Onani mutuwo |