Genesis 41:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Farao anatumiza nakaitana Yosefe; ndipo anamtulutsa iye msanga m'dzenjemo: ndipo iye anameta, nasintha malaya ake, nalowa kwa Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Farao anatumiza nakaitana Yosefe; ndipo anamtulutsa iye msanga m'dzenjemo: ndipo iye anameta, napindula malaya ake, nalowa kwa Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono Farao adaitanitsa Yosefe, ndipo adamtulutsa msanga kundendeko. Iyeyo atameta bwino ndi kusintha zovala, adapita kwa Farao kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho Farao anamuyitanitsa Yosefe, ndipo mofulumira anabwera naye kuchokera mʼdzenje muja. Ndipo atameta, ndi kusintha zovala, anapita kwa Farao. Onani mutuwo |