Genesis 41:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo panali monga momwe iye anatimasulira, momwemo mudachitika; ine anandibwezera mu utumiki wanga, mnzanga anampachika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo panali monga momwe iye anatimasulira, momwemo mudachitika; ine anandibwezera mu utumiki wanga, mnzanga anampachika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndipo zidachitikadi monga momwe adaatimasulira. Ine ndidabwerera pa ntchito yanga, koma wophika buledi uja adampachika pa mtengo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo zinthu zinachitikadi monga mmene anatitanthauzira. Ine anandibwezera pa ntchito yanga ndipo winayo anapachikidwa.” Onani mutuwo |