Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 41:10 - Buku Lopatulika

10 Farao anakwiya ndi anyamata ake, nandiika ine ndisungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, ine ndi wophika mkate wamkulu:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Farao anakwiya ndi anyamata ake, nandiika ine ndisungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, ine ndi wophika mkate wamkulu:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Paja inu mfumu mudaatipsera mtima antchitofe. Ndipo ine ndi wophika buledi tonse mudaatitsekera m'ndende, m'nyumba ya mkulu wa alonda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Paja nthawi ina Farao anapsera mtima antchito akefe, ndipo anatitsekera (ine ndi mkulu wa ophika buledi) mʼndende, mʼnyumba ya mkulu wa alonda.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 41:10
3 Mawu Ofanana  

Amidiyani ndipo anamgulitsa iye anke ku Ejipito kwa Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda.


Ndipo mbuyake wa Yosefe anamtenga iye namuika m'kaidi, umo anamangidwa akaidi a mfumu: ndipo iye anali m'mwemo m'kaidimo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa