Genesis 41:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo wopereka chikho wamkulu anati kwa Farao, kuti, Ine ndidzakumbukira zochimwa zanga lero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo wopereka chikho wamkulu anati kwa Farao, kuti, Ine ndidzakumbukira zochimwa zanga lero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pomwepo woperekera vinyo uja adauza Farao kuti, “Lero ndiwulule kulakwa kwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo mkulu wa operekera zakumwa anati kwa Farao, “Lero ndakumbukira kulephera kwanga. Onani mutuwo |