Genesis 41:11 - Buku Lopatulika11 ndipo tinalota loto usiku umodzi ine ndi iye; tinalota munthu yense monga mwa kumasulira kwa loto lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo tinalota loto usiku umodzi ine ndi iye; tinalota munthu yense monga mwa kumasulira kwa loto lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono usiku wina, aŵirife tidaalota maloto. Aliyense mwa ife anali atalota maloto ake, a tanthauzo lakelake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsiku lina tonse awiri tinalota maloto, ndipo loto lililonse linali ndi tanthauzo lake. Onani mutuwo |