Genesis 41:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali zitapita zaka ziwiri zamphumphu, Farao analota; ndipo, taonani, anaima pamtsinje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali zitapita zaka ziwiri zamphumphu, Farao analota; ndipo, taonani, anaima panyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Patapita zaka ziŵiri, Farao adaalota kuti waimirira pamphepete pa mtsinje wa Nailo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita zaka ziwiri zathunthu, Farao analota atayimirira mʼmbali mwa mtsinje wa Nailo, Onani mutuwo |