Genesis 40:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo analota maloto onse awiri, yense loto lake, usiku umodzi, yense monga mwa kumasulira kwa loto lake, wopereka chikho ndi wophika mkate wa mfumu ya Aejipito, amene anamangidwa m'kaidi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo analota maloto onse awiri, yense loto lake, usiku umodzi, yense monga mwa kumasulira kwa loto lake, wopereka chikho ndi wophika mkate wa mfumu ya Aejipito, amene anamangidwa m'kaidi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Usiku wina m'ndendemo, anthu aŵiri onse aja, woperekera vinyo uja ndi wophika buledi, adalota maloto. Aliyense mwa aŵiriwo adalota maloto ake a tanthauzo lakelake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Usiku wina, aliyense wa anthu awiriwa, wopereka zakumwa pamodzi ndi wopanga buledi wa ku nyumba ya mfumu ya ku Igupto aja, amene ankasungidwa mʼndende, analota maloto. Malotowo anali ndi tanthauzo lake. Onani mutuwo |