Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 40:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo kazembe wa alonda anapereka iwo kwa Yosefe, ndipo iye anawatumikira iwo: ndipo anakhala nthawi mosungidwamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo kazembe wa alonda anapereka iwo kwa Yosefe, ndipo iye anawatumikira iwo: ndipo anakhala nthawi mosungidwamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Mkulu wa alonda uja adasankhula Yosefe kuti asamalire anthu aŵiriwo ndi kuŵalonda. Adakhalamo nthaŵi yaitali ndithu m'ndendemo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mkulu wa alonda aja anawapereka mʼmanja mwa Yosefe, ndipo iye anawasamalira. Iwo anakhala mʼndendemo kwa kanthawi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 40:4
7 Mawu Ofanana  

Amidiyani ndipo anamgulitsa iye anke ku Ejipito kwa Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda.


Ndipo anatsika naye Yosefe kunka ku Ejipito; ndipo Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda, Mwejipito, anamgula iye m'manja mwa Aismaele amene anatsika naye kunka kumeneko.


Ndipo anaika iwo asungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, m'kaidi, umo anamangidwa Yosefe.


Ndipo analota maloto onse awiri, yense loto lake, usiku umodzi, yense monga mwa kumasulira kwa loto lake, wopereka chikho ndi wophika mkate wa mfumu ya Aejipito, amene anamangidwa m'kaidi.


Ndipo anaika onse m'kaidi masiku atatu.


Pereka njira yako kwa Yehova; khulupiriranso Iye, adzachichita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa