Genesis 40:22 - Buku Lopatulika22 Koma anampachika wophika mkate wamkulu; monga Yosefe anawamasulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Koma anampachika wophika mkate wamkulu; monga Yosefe anawamasulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Koma wophika buledi uja adampachika, monga momwe Yosefe adaanenera pomasulira maloto ao aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 koma mkulu wa ophika buledi anamupachika, mofanana ndi mmene Yosefe anatanthauzira maloto. Onani mutuwo |