Genesis 40:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anabwezanso wopereka chikho ku ntchito yake; ndipo iye anapereka chikho m'manja a Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anabwezanso wopereka chikho ku ntchito yake; ndipo iye anapereka chikho m'manja a Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Farao adamubwezera pa tchito yake woperekera vinyo uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsono Farao anamubwezera mkulu wa operekera zakumwa uja pa udindo wake, kotero kuti anayamba kuperekeranso zakumwa kwa Farao, Onani mutuwo |