Genesis 40:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yosefe anayankha nati, Kumasulira kwake ndi uku: malichero atatu ndiwo masiku atatu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yosefe anayankha nati, Kumasulira kwake ndi uku: malichero atatu ndiwo masiku atatu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Yosefe adamuyankha kuti, “Kamasulidwe kake ka maloto ameneŵa ndi aka: nsengwa zitatu ndi masiku atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yosefe anati, “Tanthauzo lake ndi ili: nsengwa zitatuzo ndi masiku atatu. Onani mutuwo |