Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 40:17 - Buku Lopatulika

17 m'lichero lapamwamba munali mikate ya Farao ya mitundumitundu; ndipo mbalame zinadya ya m'lichero la pamutu panga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 m'lichero lapamwamba munali mikate ya Farao ya mitundumitundu; ndipo mbalame zinadya ya m'lichero la pamutu panga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 M'nsengwa yapamwamba munali mitundu yambiri ya chakudya cha Farao, koma mbalame zinalikudya chakudyacho.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Mu nsengwa yapamwamba munali zakudya zamitundumitundu za Farao, koma mbalame zimadya zakudyazo.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 40:17
4 Mawu Ofanana  

Pamene wophika mkate anaona kuti kumasulira kwake kunali kwabwino, iye anati kwa Yosefe, Inenso ndinalimkulota, ndipo, taonani, malichero atatu a mikate yoyera anali pamutu panga;


Ndipo Yosefe anayankha nati, Kumasulira kwake ndi uku: malichero atatu ndiwo masiku atatu;


Ndi Asere, chakudya chake ndicho mafuta, ndipo adzapereka zolongosoka zachifumu.


Pomuka iye ku Zikilagi anapatukira kwa iye a Manase: Adina, ndi Yozabadi, ndi Yediyaele, ndi Mikaele, ndi Yozabadi, ndi Elihu, ndi Ziletai, akulu a zikwi a ku Manase.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa