Genesis 40:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yosefe anati kwa iye, Kumasulira kwake ndi uwu: nthambi zitatu ndizo masiku atatu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yosefe anati kwa iye, Kumasulira kwake ndi uwu: nthambi zitatu ndizo masiku atatu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Yosefe adamuyankha kuti, “Tanthauzo lake la maloto ameneŵa nali: nthambi zitatuzo ndi masiku atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yosefe anati kwa iye, “Tanthauzo lake ndi ili: Nthambi zitatuzo ndi masiku atatu. Onani mutuwo |