Genesis 40:11 - Buku Lopatulika11 ndipo chikho cha Farao chinali m'dzanja langa: ndipo ndinatenga mphesa, ndi kufinyira m'chikho cha Farao ndi kupereka chikho m'dzanja la Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo chikho cha Farao chinali m'dzanja langa: ndipo ndinatenga mphesa, ndi kufinyira m'chikho cha Farao ndi kupereka chikho m'dzanja la Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Chikho cha Farao chinali m'manja mwanga; ine ndinatenga mphesazo nkufinyira m'chikhomo, ndipo ndinachipereka kwa Farao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Chikho cha Farao chinali mʼmanja mwanga, ndipo ndinatenga mphesa, kupsinyira mu chikho cha Farao ndi kuchipereka mʼmanja mwake.” Onani mutuwo |