Genesis 4:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yehova anati kwa Kaini, Ukwiyiranji? Yagweranji nkhope yako? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yehova anati kwa Kaini, Ukwiyiranji? Yagweranji nkhope yako? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Apo Chauta adafunsa Kainiyo kuti, “Kodi wakwiyiranji chotere? Chifukwa chiyani nkhope yako yagwa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Yehova anati kwa Kaini, “Chifukwa chiyani wakwiya ndipo bwanji nkhope yako yagwa? Onani mutuwo |