Genesis 4:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Ada anabala Yabala; iye ndiye atate wao wa iwo okhala m'mahema, akuweta ng'ombe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Ada anabala Yabala; iye ndiye atate wao wa iwo okhala m'mahema, akuweta ng'ombe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ada adabala Yabala, ndipo iyeyu ndiye kholo la onse oŵeta zoŵeta ndi okhala m'mahema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ada anabereka Yabala; iyeyu anali kholo la onse okhala mʼmatenti ndi oweta ziweto. Onani mutuwo |