Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 4:21 - Buku Lopatulika

21 Ndi dzina la mphwake ndilo Yubala; iye ndiye atate wao wa iwo oimba zeze ndi chitoliro.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndi dzina la mphwake ndilo Yubale; iye ndiye atate wao wa iwo oimba zeze ndi chitoliro.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Mbale wake anali Yubale, ndipo ndiye kholo la onse okhoza kuimba zeze ndi toliro.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Dzina la mʼbale wake linali Yubala; iyeyu anali kholo la onse oyimba zeze ndi chitoliro.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 4:21
8 Mawu Ofanana  

Wathawanji iwe mobisika, ndi kundichokera kuseri, osandiuza ine, kuti ndikadakumukitsa iwe ndi kusekerera ndi nyimbo ndi lingaka ndi zeze?


Ndipo Ada anabala Yabala; iye ndiye atate wao wa iwo okhala m'mahema, akuweta ng'ombe.


Ndipo Zila, iyenso anabala Tubala-Kaini, mwini wakuphunzitsa amisiri onse a mkuwa ndi a chitsulo; mlongo wake wa Tubala-Kaini ndi Naama.


Aimbira lingaka ndi zeze, nakondwera pomveka chitoliro.


Mlemekezeni ndi lingaka ndi kuthira mang'ombe: Mlemekezeni ndi zoimbira za zingwe ndi chitoliro.


Ndipo zeze ndi mngoli, ndi lingaka ndi chitoliro, ndi vinyo, zili m'maphwando ao; koma iwo sapenyetsa ntchito ya Yehova; ngakhale kuyang'ana pa machitidwe a manja ake.


akungoimba kutsata maliridwe a zeze, nadzilingiririra zoimbira nazo ngati Davide;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa