Genesis 39:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yehova anali ndi Yosefe; ndipo iye anali wolemeralemera; nakhala m'nyumba ya mbuyake Mwejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yehova anali ndi Yosefe; ndipo iye anali wolemeralemera; nakhala m'nyumba ya mbuyake Mwejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chauta anali naye Yosefe, ndipo adamthandiza kuti zonse zimuyendere bwino. Adakhala m'nyumba ya bwana wake, Mwejipito uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Yehova anali ndi Yosefe ndipo zake zonse zimayenda bwino. Iye ankakhala mʼnyumba ya mbuye wake wa ku Igupto. Onani mutuwo |