Genesis 39:18 - Buku Lopatulika18 ndipo panali pamene ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chovala chake kwa ine, nathawira kunja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndipo panali pamene ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chovala chake kwa ine, nathawira kunja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Koma ine nditakuwa, iyeyo anasiya mwinjiro wake pafupi ndi ine, nkuthaŵira pabwalo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Koma pamene ndinakuwa, iye anandisiyira mkanjo wake nathawira kunja.” Onani mutuwo |