Genesis 39:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo ananena kwa iye monga mau awa, anati, Analowa kwa ine kapolo wa Chihebri uja, munabwera naye kwathu, kundipunza ine: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo ananena kwa iye monga mau awa, anati, Analowa kwa ine kapolo wa Chihebri uja, munabwera naye kwathu, kundipunza ine: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono atabwera, adamsimbira nkhani yonseyo, adati, “Kapolo uja Wachihebri mudabwera naye m'nyumba munoyu, analoŵa kuchipinda kwanga kukandipunza ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Tsono anamuwuza nkhaniyi nati: “Wantchito Wachihebri amene munatibweretsera uja anabwera kuti adzagone nane. Onani mutuwo |