Genesis 39:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anasunga chofunda chake chikhale ndi iye kufikira atabwera kwao mbuyake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anasunga chofunda chake chikhale ndi iye kufikira atabwera kwao mbuyake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mwinjirowo adangousunga m'manja kudikira mpaka bwana wa Yosefe atabwera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Tsono mkazi wa Potifara uja anasunga mkanjowo mpaka mbuye wake wa Yosefe atabwera ku nyumba. Onani mutuwo |