Genesis 39:15 - Buku Lopatulika15 ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chofunda chake kwa ine nathawira kubwalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chofunda chake kwa ine nathawira kubwalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono atamva kukuwa kwangako, wasiya mwinjiro wake m'manja mwangamu nkuthaŵira pabwalo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Atandimva ndikukuwa, anandisiyira mkanjo wakewu nʼkuthawira kunja.” Onani mutuwo |