Genesis 38:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Onani anadziwa kuti mbeu siidzakhala yake: ndipo panali pamene iye analowana naye mkazi wa mbale wake, kuti anaitaya pansi, kuti angampatse mbeu kwa mkulu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Onani anadziwa kuti mbeu siidzakhala yake: ndipo panali pamene iye analowana naye mkazi wa mbale wake, kuti anaitaya pansi, kuti angampatse mbeu kwa mkulu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Onani adaadziŵa kuti anawo sadzakhala ake. Motero nthaŵi zonse akamakhala naye mkaziyo, ankangotayira pansi mbeu yake, kuti asamubalire ana mbale wakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Onani anadziwa kuti mwanayo sadzakhala wake. Choncho nthawi zonse pamene amagona naye mkaziyo, ankatayira umuna pansi kuti asamuberekere mwana mʼbale wake. Onani mutuwo |