Genesis 38:10 - Buku Lopatulika10 Koma chimene iye anachita chinali choipa pamaso pa Yehova, ndipo anamupha iyenso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma chimene iye anachita chinali choipa pamaso pa Yehova, ndipo anamupha iyenso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono zimene ankachitazo zidaipira Chauta ndipo Chauta adamlanganso ndi imfa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Zimene ankachitazi zinayipira Yehova. Choncho anamulanganso ndi imfa. Onani mutuwo |