Genesis 38:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Yuda anati kwa Tamara mpongozi wake, Khala wamasiye m'nyumba ya atate wako, kufikira akakula msinkhu Sela mwana wanga wamwamuna: chifukwa anati kuti, Angafe iyenso monga abale ake. Ndipo Tamara ananka nakhala m'nyumba ya atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Yuda anati kwa Tamara mpongozi wake, Khala wamasiye m'nyumba ya atate wako, kufikira akakula msinkhu Sela mwana wanga wamwamuna: chifukwa anati kuti, Angafe iyenso monga abale ake. Ndipo Tamara ananka nakhala m'nyumba ya atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Apo Yuda adauza mpongozi wake uja Tamara kuti, “Bwererani kunyumba kwa bambo wanu, mukakhale wamasiye kumeneko mpaka mwana wanga Sela atakula.” Adanena zimenezi chifukwa ankaopa kuti Sela angafenso monga abale akewo. Motero Tamara adabwerera kunyumba kwa bambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka Yuda anati kwa mpongozi wake Tamara, “Bwererani ku nyumba ya abambo anu ndi kukhala kumeneko ngati wamasiye mpaka mwana wanga Sela atakula.” Ananena izi chifukwa ankaopa kuti Sela angafenso ngati abale ake aja. Choncho Tamara anapita kukakhala ku nyumba ya abambo ake. Onani mutuwo |