Genesis 38:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yuda anamtengera Eri mwana wake woyamba mkazi, ndipo dzina lake ndilo Tamara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yuda anamtengera Eri mwana wake woyamba mkazi, ndipo dzina lake ndilo Tamara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yuda adampezera mkazi mwana wake wachisamba uja Ere, dzina lake Tamara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yuda anamupezera mkazi mwana wake woyamba uja Eri, ndipo dzina la mkaziyo linali Tamara. Onani mutuwo |