Genesis 38:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Eri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Eri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mkaziyo adatenga pathupi nabala mwana wamwamuna, nkumutcha Ere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye anatenga pathupi, nabala mwana wamwamuna amene anamutcha Eri. Onani mutuwo |